Ekisodo 27:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Ziwiya zonse zogwiritsa ntchito pa utumiki wonse wapachihema, zikhomo zake zonse ndi zikhomo zonse za nsalu yampanda wa bwalolo zikhale zakopa.+
19 Ziwiya zonse zogwiritsa ntchito pa utumiki wonse wapachihema, zikhomo zake zonse ndi zikhomo zonse za nsalu yampanda wa bwalolo zikhale zakopa.+