Levitiko 15:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uza Aisiraeli kuti, ‘Ngati mwamuna ali ndi nthenda ya kukha kumaliseche, nthenda yakeyo ikumupangitsa kukhala wodetsedwa.+
2 “Uza Aisiraeli kuti, ‘Ngati mwamuna ali ndi nthenda ya kukha kumaliseche, nthenda yakeyo ikumupangitsa kukhala wodetsedwa.+