Levitiko 21:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Yehova anapitiriza kulankhula ndi Mose kuti: “Uza ansembe, ana a Aroni kuti, ‘Aliyense wa inu asadzidetse chifukwa cha munthu amene wamwalira pakati pa anthu a mtundu wake.+ Levitiko 21:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Iye asayandikire munthu aliyense wakufa+ ndipo asamadzidetse ngakhale amene wamwalirayo atakhala bambo ake kapena mayi ake.
21 Yehova anapitiriza kulankhula ndi Mose kuti: “Uza ansembe, ana a Aroni kuti, ‘Aliyense wa inu asadzidetse chifukwa cha munthu amene wamwalira pakati pa anthu a mtundu wake.+
11 Iye asayandikire munthu aliyense wakufa+ ndipo asamadzidetse ngakhale amene wamwalirayo atakhala bambo ake kapena mayi ake.