-
Levitiko 5:8Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
8 Azibweretsa mbalamezi kwa wansembe, ndipo wansembeyo azipereka nsembe yamachimo choyamba, ataicheka pakhosi koma osaduliratu mutu wake.
-