-
Rute 2:4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
4 Pasanapite nthawi, Boazi anafika kuchokera ku Betelehemu ndipo analonjera okololawo kuti: “Yehova akhale nanu.” Iwo anayankha kuti: “Yehova akudalitseni.”
-
-
Salimo 134:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Yehova, amene anapanga kumwamba ndi dziko lapansi,
Akudalitseni ali ku Ziyoni.
-