1 Mafumu 8:63 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 63 Solomo anapereka nsembe zamgwirizano+ kwa Yehova. Anapereka ngʼombe 22,000 ndi nkhosa 120,000. Choncho mfumuyo ndi Aisiraeli onse anatsegulira nyumba ya Yehova.+ 2 Mbiri 7:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mfumu Solomo inapereka nsembe ngʼombe 22,000 ndi nkhosa 120,000. Choncho mfumuyo ndi anthu onse anatsegulira nyumba ya Mulungu woona.+
63 Solomo anapereka nsembe zamgwirizano+ kwa Yehova. Anapereka ngʼombe 22,000 ndi nkhosa 120,000. Choncho mfumuyo ndi Aisiraeli onse anatsegulira nyumba ya Yehova.+
5 Mfumu Solomo inapereka nsembe ngʼombe 22,000 ndi nkhosa 120,000. Choncho mfumuyo ndi anthu onse anatsegulira nyumba ya Mulungu woona.+