Numeri 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mutenge amuna ena kuti akuthandizeni. Mutenge mwamuna mmodzi pafuko lililonse ndipo akhale mtsogoleri wa nyumba ya makolo ake.+ Numeri 1:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 kuchokera ku fuko la Yuda, Naasoni+ mwana wa Aminadabu, Numeri 2:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Amene azimanga msasa wawo kumʼmawa kotulukira dzuwa ndi gulu la mafuko atatu la Yuda ndi magulu awo.* Mtsogoleri wa ana a Yuda ndi Naasoni,+ mwana wa Aminadabu. Rute 4:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Aminadabu+ anabereka Naasoni, Naasoni anabereka Salimoni, Mateyu 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ramu anabereka Aminadabu.Aminadabu anabereka Naasoni.+Naasoni anabereka Salimoni.
4 Mutenge amuna ena kuti akuthandizeni. Mutenge mwamuna mmodzi pafuko lililonse ndipo akhale mtsogoleri wa nyumba ya makolo ake.+
3 Amene azimanga msasa wawo kumʼmawa kotulukira dzuwa ndi gulu la mafuko atatu la Yuda ndi magulu awo.* Mtsogoleri wa ana a Yuda ndi Naasoni,+ mwana wa Aminadabu.