Numeri 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mutenge amuna ena kuti akuthandizeni. Mutenge mwamuna mmodzi pafuko lililonse ndipo akhale mtsogoleri wa nyumba ya makolo ake.+ Numeri 1:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 kuchokera ku fuko la Isakara, Netaneli+ mwana wa Zuwara, Numeri 2:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pafupi ndi fuko limeneli kuzikhala fuko la Isakara. Mtsogoleri wa ana a Isakara ndi Netaneli,+ mwana wa Zuwara. Numeri 10:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Mtsogoleri wa gulu la fuko la ana a Isakara anali Netaneli,+ mwana wa Zuwara.
4 Mutenge amuna ena kuti akuthandizeni. Mutenge mwamuna mmodzi pafuko lililonse ndipo akhale mtsogoleri wa nyumba ya makolo ake.+
5 Pafupi ndi fuko limeneli kuzikhala fuko la Isakara. Mtsogoleri wa ana a Isakara ndi Netaneli,+ mwana wa Zuwara.