Numeri 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mutenge amuna ena kuti akuthandizeni. Mutenge mwamuna mmodzi pafuko lililonse ndipo akhale mtsogoleri wa nyumba ya makolo ake.+ Numeri 1:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 kuchokera ku fuko la Simiyoni, Selumiyeli+ mwana wa Zurisadai,
4 Mutenge amuna ena kuti akuthandizeni. Mutenge mwamuna mmodzi pafuko lililonse ndipo akhale mtsogoleri wa nyumba ya makolo ake.+