Ekisodo 33:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mose akangolowa mʼchihema, chipilala cha mtambo+ chinkatsika nʼkuima pakhomo la chihemacho pa nthawi imene Mulungu akulankhula ndi Mose.+ Numeri 11:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Ine ndibwera kumeneko+ kudzalankhula nawe+ ndipo ndidzatenga gawo lina la mzimu+ umene uli pa iwe nʼkuuika pa anthuwo. Pamenepo iwo adzatha kukuthandiza kusenza udindo woyangʼanira anthuwo, kuti usausenze wekha.+ Numeri 12:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndimalankhula naye pamasomʼpamaso,*+ kumuuza zinthu momveka bwino osati mophiphiritsa, ndipo amaona maonekedwe a Yehova. Ndiye nʼchifukwa chiyani inu simunaope kumunena Mose mtumiki wanga?”
9 Mose akangolowa mʼchihema, chipilala cha mtambo+ chinkatsika nʼkuima pakhomo la chihemacho pa nthawi imene Mulungu akulankhula ndi Mose.+
17 Ine ndibwera kumeneko+ kudzalankhula nawe+ ndipo ndidzatenga gawo lina la mzimu+ umene uli pa iwe nʼkuuika pa anthuwo. Pamenepo iwo adzatha kukuthandiza kusenza udindo woyangʼanira anthuwo, kuti usausenze wekha.+
8 Ndimalankhula naye pamasomʼpamaso,*+ kumuuza zinthu momveka bwino osati mophiphiritsa, ndipo amaona maonekedwe a Yehova. Ndiye nʼchifukwa chiyani inu simunaope kumunena Mose mtumiki wanga?”