Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 30:18, 19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 “Upange beseni losambira lakopa+ ndi choikapo chake. Ukatero uliike pakati pa chihema chokumanako ndi guwa lansembe ndipo uthiremo madzi.+ 19 Aroni ndi ana ake azisamba mʼmanja ndi mapazi awo pamenepo.+

  • Levitiko 16:28
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 28 Munthu amene wawotcha zimenezi azichapa zovala zake nʼkusamba thupi lonse, akatero angathe kulowa mumsasa.

  • Numeri 19:7
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 Akatha, wansembeyo achape zovala zake nʼkusamba* ndi madzi. Pambuyo pake akhoza kulowa mumsasa, koma adzakhala wodetsedwa mpaka madzulo.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena