Ekisodo 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Ndipatulireni* mwana aliyense wamwamuna woyamba kubadwa,* wa munthu ndi wa chiweto, pakati pa Aisiraeli. Ameneyu ndi wanga.”+ Ekisodo 13:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 muzidzapereka kwa Yehova mwana aliyense wamwamuna woyamba kubadwa,* wa munthu komanso wa chiweto. Chachimuna chilichonse ndi cha Yehova.+ Levitiko 27:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Koma munthu asapereke nyama iliyonse yoyamba kubadwa kuti ikhale yopatulika, chifukwa iliyonse yoyamba kubadwa ndi ya Yehova.+ Kaya ndi ngʼombe kapena nkhosa, ndi za Yehova.+
2 “Ndipatulireni* mwana aliyense wamwamuna woyamba kubadwa,* wa munthu ndi wa chiweto, pakati pa Aisiraeli. Ameneyu ndi wanga.”+
12 muzidzapereka kwa Yehova mwana aliyense wamwamuna woyamba kubadwa,* wa munthu komanso wa chiweto. Chachimuna chilichonse ndi cha Yehova.+
26 Koma munthu asapereke nyama iliyonse yoyamba kubadwa kuti ikhale yopatulika, chifukwa iliyonse yoyamba kubadwa ndi ya Yehova.+ Kaya ndi ngʼombe kapena nkhosa, ndi za Yehova.+