Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 12:29
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 29 Ndiyeno pakati pa usiku, Yehova anapha mwana aliyense woyamba kubadwa mʼdziko la Iguputo.+ Kuyambira mwana woyamba wa Farao, amene anali pampando wachifumu, mpaka mwana woyamba wa mkaidi amene anali mʼndende, ndiponso mwana aliyense woyamba kubadwa wa nyama.+

  • Ekisodo 13:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Farao atakana mouma mtima kuti tichoke,+ Yehova anapha mwana woyamba kubadwa aliyense mʼdziko la Iguputo, kuyambira mwana woyamba kubadwa wa munthu mpaka mwana woyamba kubadwa wa nyama.+ Nʼchifukwa chake tikupereka nsembe kwa Yehova ana onse a nyama oyamba kubadwa* ndiponso tikuwombola mwana wathu wamwamuna aliyense woyamba kubadwa.’

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena