Numeri 1:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Alevi azimanga matenti awo mozungulira chihema cha Umboni kuti mkwiyo wa Mulungu usayakire Aisiraeli.+ Aleviwo ndi amene ali ndi udindo wosamalira* chihema cha Umbonicho.”+ Numeri 3:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Mkulu wa atsogoleri onse a Alevi anali Eleazara,+ mwana wa wansembe Aroni. Iye ndi amene ankayangʼanira anthu onse amene ankatumikira pamalo oyera. Numeri 18:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Azikuthandizani komanso azigwira ntchito zawo zonse zapachihema chokumanako, ndipo munthu wamba* aliyense asamayandikire kwa inu.+
53 Alevi azimanga matenti awo mozungulira chihema cha Umboni kuti mkwiyo wa Mulungu usayakire Aisiraeli.+ Aleviwo ndi amene ali ndi udindo wosamalira* chihema cha Umbonicho.”+
32 Mkulu wa atsogoleri onse a Alevi anali Eleazara,+ mwana wa wansembe Aroni. Iye ndi amene ankayangʼanira anthu onse amene ankatumikira pamalo oyera.
4 Azikuthandizani komanso azigwira ntchito zawo zonse zapachihema chokumanako, ndipo munthu wamba* aliyense asamayandikire kwa inu.+