Ekisodo 12:46 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 46 Muzidyera mʼnyumba imodzi. Musatuluke panja ndi nyama iliyonse komanso musaphwanye fupa lililonse la nyamayo.+ Salimo 34:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Amateteza mafupa onse a munthu wolungamayo.Ndipo palibe fupa ngakhale limodzi limene lathyoledwa.+ Yohane 19:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Kwenikweni zimenezi zinachitika kuti lemba likwaniritsidwe, limene limati: “Sadzathyola* fupa lake ndi limodzi lomwe.”+
46 Muzidyera mʼnyumba imodzi. Musatuluke panja ndi nyama iliyonse komanso musaphwanye fupa lililonse la nyamayo.+
20 Amateteza mafupa onse a munthu wolungamayo.Ndipo palibe fupa ngakhale limodzi limene lathyoledwa.+
36 Kwenikweni zimenezi zinachitika kuti lemba likwaniritsidwe, limene limati: “Sadzathyola* fupa lake ndi limodzi lomwe.”+