Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 12:19
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 19 Kwa masiku 7 mʼnyumba zanu musamadzapezeke ufa wokanda wokhala ndi zofufumitsa, chifukwa aliyense amene wadya chakudya chokhala ndi zofufumitsa, kaya ndi mlendo kapena mbadwa ya Isiraeli,+ munthu ameneyo adzaphedwa kuti asakhalenso pagulu la Isiraeli.+

  • Ekisodo 12:48
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 48 Ngati mlendo amene akukhala nanu akufuna kuchita nawo chikondwerero cha Pasika kwa Yehova, mwamuna aliyense wamʼnyumba yake adulidwe. Akatero angathe kubwera kudzachita nawo chikondwererocho, ndipo ayenera kuonedwa ngati mbadwa ya dzikolo. Koma munthu wosadulidwa asadye nawo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena