2 Mbiri 13:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiye tamverani! Mulungu woona ali nafe ndipo akutitsogolera ndi ansembe ake ndiponso malipenga otiitanira ku nkhondo yomenyana nanu. Inu Aisiraeli, musamenyane ndi Yehova Mulungu wa makolo anu chifukwa simupambana.”+
12 Ndiye tamverani! Mulungu woona ali nafe ndipo akutitsogolera ndi ansembe ake ndiponso malipenga otiitanira ku nkhondo yomenyana nanu. Inu Aisiraeli, musamenyane ndi Yehova Mulungu wa makolo anu chifukwa simupambana.”+