Numeri 1:4, 5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mutenge amuna ena kuti akuthandizeni. Mutenge mwamuna mmodzi pafuko lililonse ndipo akhale mtsogoleri wa nyumba ya makolo ake.+ 5 Mayina a amuna amene akuthandizeni ndi awa: kuchokera ku fuko la Rubeni, Elizuri+ mwana wa Sedeuri, Numeri 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Amene azimanga msasa wawo kumʼmwera ndi gulu la mafuko atatu la Rubeni+ ndi magulu awo.* Mtsogoleri wa ana a Rubeni ndi Elizuri,+ mwana wa Sedeuri.
4 Mutenge amuna ena kuti akuthandizeni. Mutenge mwamuna mmodzi pafuko lililonse ndipo akhale mtsogoleri wa nyumba ya makolo ake.+ 5 Mayina a amuna amene akuthandizeni ndi awa: kuchokera ku fuko la Rubeni, Elizuri+ mwana wa Sedeuri,
10 Amene azimanga msasa wawo kumʼmwera ndi gulu la mafuko atatu la Rubeni+ ndi magulu awo.* Mtsogoleri wa ana a Rubeni ndi Elizuri,+ mwana wa Sedeuri.