Numeri 1:5, 6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mayina a amuna amene akuthandizeni ndi awa: kuchokera ku fuko la Rubeni, Elizuri+ mwana wa Sedeuri, 6 kuchokera ku fuko la Simiyoni, Selumiyeli+ mwana wa Zurisadai, Numeri 2:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pafupi ndi fuko limeneli pazikhala fuko la Simiyoni. Mtsogoleri wa ana a Simiyoni ndi Selumiyeli,+ mwana wa Zurisadai.
5 Mayina a amuna amene akuthandizeni ndi awa: kuchokera ku fuko la Rubeni, Elizuri+ mwana wa Sedeuri, 6 kuchokera ku fuko la Simiyoni, Selumiyeli+ mwana wa Zurisadai,
12 Pafupi ndi fuko limeneli pazikhala fuko la Simiyoni. Mtsogoleri wa ana a Simiyoni ndi Selumiyeli,+ mwana wa Zurisadai.