Numeri 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mutenge amuna ena kuti akuthandizeni. Mutenge mwamuna mmodzi pafuko lililonse ndipo akhale mtsogoleri wa nyumba ya makolo ake.+ Numeri 1:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 kuchokera ku fuko la Gadi, Eliyasafu+ mwana wa Deyueli, Numeri 2:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Kenako pazibwera fuko la Gadi. Mtsogoleri wa ana a Gadi ndi Eliyasafu,+ mwana wa Reueli.
4 Mutenge amuna ena kuti akuthandizeni. Mutenge mwamuna mmodzi pafuko lililonse ndipo akhale mtsogoleri wa nyumba ya makolo ake.+