Numeri 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mutenge amuna ena kuti akuthandizeni. Mutenge mwamuna mmodzi pafuko lililonse ndipo akhale mtsogoleri wa nyumba ya makolo ake.+ Numeri 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pa ana a Yosefe: kuchokera ku fuko la Efuraimu,+ Elisama mwana wa Amihudi, kuchokera ku fuko la Manase, Gamaliyeli mwana wa Pedazuri, Numeri 2:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Amene azimanga msasa wawo kumadzulo ndi gulu la mafuko atatu la Efuraimu ndi magulu awo.* Mtsogoleri wa ana a Efuraimu ndi Elisama,+ mwana wa Amihudi. Numeri 2:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Asilikali onse a gulu la Efuraimu amene anawalemba mayina alipo 108,100. Amenewa azikhala achitatu kunyamuka.+
4 Mutenge amuna ena kuti akuthandizeni. Mutenge mwamuna mmodzi pafuko lililonse ndipo akhale mtsogoleri wa nyumba ya makolo ake.+
10 Pa ana a Yosefe: kuchokera ku fuko la Efuraimu,+ Elisama mwana wa Amihudi, kuchokera ku fuko la Manase, Gamaliyeli mwana wa Pedazuri,
18 Amene azimanga msasa wawo kumadzulo ndi gulu la mafuko atatu la Efuraimu ndi magulu awo.* Mtsogoleri wa ana a Efuraimu ndi Elisama,+ mwana wa Amihudi.
24 Asilikali onse a gulu la Efuraimu amene anawalemba mayina alipo 108,100. Amenewa azikhala achitatu kunyamuka.+