Numeri 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mutenge amuna ena kuti akuthandizeni. Mutenge mwamuna mmodzi pafuko lililonse ndipo akhale mtsogoleri wa nyumba ya makolo ake.+ Numeri 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Pa ana a Yosefe: kuchokera ku fuko la Efuraimu,+ Elisama mwana wa Amihudi, kuchokera ku fuko la Manase, Gamaliyeli mwana wa Pedazuri, Numeri 2:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pafupi ndi fuko limeneli pazibwera fuko la Manase.+ Mtsogoleri wa ana a Manase ndi Gamaliyeli,+ mwana wa Pedazuri.
4 Mutenge amuna ena kuti akuthandizeni. Mutenge mwamuna mmodzi pafuko lililonse ndipo akhale mtsogoleri wa nyumba ya makolo ake.+
10 Pa ana a Yosefe: kuchokera ku fuko la Efuraimu,+ Elisama mwana wa Amihudi, kuchokera ku fuko la Manase, Gamaliyeli mwana wa Pedazuri,
20 Pafupi ndi fuko limeneli pazibwera fuko la Manase.+ Mtsogoleri wa ana a Manase ndi Gamaliyeli,+ mwana wa Pedazuri.