Numeri 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mutenge amuna ena kuti akuthandizeni. Mutenge mwamuna mmodzi pafuko lililonse ndipo akhale mtsogoleri wa nyumba ya makolo ake.+ Numeri 1:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 kuchokera ku fuko la Benjamini, Abidana+ mwana wa Gidiyoni, Numeri 2:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Kenako pazibwera fuko la Benjamini. Mtsogoleri wa ana a Benjamini ndi Abidana,+ mwana wa Gidiyoni.
4 Mutenge amuna ena kuti akuthandizeni. Mutenge mwamuna mmodzi pafuko lililonse ndipo akhale mtsogoleri wa nyumba ya makolo ake.+
22 Kenako pazibwera fuko la Benjamini. Mtsogoleri wa ana a Benjamini ndi Abidana,+ mwana wa Gidiyoni.