Numeri 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mutenge amuna ena kuti akuthandizeni. Mutenge mwamuna mmodzi pafuko lililonse ndipo akhale mtsogoleri wa nyumba ya makolo ake.+ Numeri 1:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 kuchokera ku fuko la Aseri, Pagiyeli+ mwana wa Okirani, Numeri 2:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Pafupi ndi fuko limeneli pazibwera fuko la Aseri. Mtsogoleri wa ana a Aseri ndi Pagiyeli,+ mwana wa Okirani.
4 Mutenge amuna ena kuti akuthandizeni. Mutenge mwamuna mmodzi pafuko lililonse ndipo akhale mtsogoleri wa nyumba ya makolo ake.+
27 Pafupi ndi fuko limeneli pazibwera fuko la Aseri. Mtsogoleri wa ana a Aseri ndi Pagiyeli,+ mwana wa Okirani.