Numeri 1:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Mutenge amuna ena kuti akuthandizeni. Mutenge mwamuna mmodzi pafuko lililonse ndipo akhale mtsogoleri wa nyumba ya makolo ake.+ Numeri 1:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 kuchokera ku fuko la Nafitali, Ahira+ mwana wa Enani. Numeri 2:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Kenako pazibwera fuko la Nafitali. Mtsogoleri wa ana a Nafitali ndi Ahira,+ mwana wa Enani.
4 Mutenge amuna ena kuti akuthandizeni. Mutenge mwamuna mmodzi pafuko lililonse ndipo akhale mtsogoleri wa nyumba ya makolo ake.+