Numeri 2:34 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 34 Aisiraeli anachita zonse mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose. Dongosolo limene analitsatira pomanga misasa yawo mʼmagulu a mafuko atatu,+ ndi limenenso anatsatira posamuka,+ aliyense mʼbanja lake mogwirizana ndi nyumba ya makolo ake.
34 Aisiraeli anachita zonse mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose. Dongosolo limene analitsatira pomanga misasa yawo mʼmagulu a mafuko atatu,+ ndi limenenso anatsatira posamuka,+ aliyense mʼbanja lake mogwirizana ndi nyumba ya makolo ake.