-
Yoswa 3:3, 4Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 ndipo anauza anthuwo kuti: “Mukangoona likasa la pangano la Yehova Mulungu wanu litanyamulidwa ndi Alevi omwe ndi ansembe,+ musamuke pamalo panu nʼkuyamba kulitsatira, 4 koma musaliyandikire. Pakati pa inu ndi likasalo pakhale mtunda wokwana mikono pafupifupi 2,000.* Mukatero mudzadziwa koyenera kupita, chifukwa kumeneko simunayambe mwapitako.”
-