Ekisodo 33:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Mose akangolowa mʼchihema, chipilala cha mtambo+ chinkatsika nʼkuima pakhomo la chihemacho pa nthawi imene Mulungu akulankhula ndi Mose.+ Numeri 12:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ndiyeno Yehova anatsika mʼchipilala chamtambo+ nʼkuima pakhomo la chihema chokumanako. Kenako anaitana Aroni ndi Miriamu ndipo onse anapita. Deuteronomo 31:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno Yehova anaonekera kuchihemako mʼchipilala cha mtambo chimene chinaima pafupi ndi khomo la chihema.+
9 Mose akangolowa mʼchihema, chipilala cha mtambo+ chinkatsika nʼkuima pakhomo la chihemacho pa nthawi imene Mulungu akulankhula ndi Mose.+
5 Ndiyeno Yehova anatsika mʼchipilala chamtambo+ nʼkuima pakhomo la chihema chokumanako. Kenako anaitana Aroni ndi Miriamu ndipo onse anapita.
15 Ndiyeno Yehova anaonekera kuchihemako mʼchipilala cha mtambo chimene chinaima pafupi ndi khomo la chihema.+