Maliko 9:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Kenako Yohane anauza Yesu kuti: “Mphunzitsi, ife tinaona munthu wina akutulutsa ziwanda mʼdzina lanu ndiye tinamuletsa, chifukwa sakuyenda ndi ife.”+
38 Kenako Yohane anauza Yesu kuti: “Mphunzitsi, ife tinaona munthu wina akutulutsa ziwanda mʼdzina lanu ndiye tinamuletsa, chifukwa sakuyenda ndi ife.”+