-
Genesis 31:10, 11Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Pa nthawi imene ziweto zinali zokonzeka kutenga bere, ndinalota maloto ndipo ndinaona mbuzi zamphongo zikukwera zazikazi. Mbuzi zamphongozo zinali zamizeremizere, zamawangamawanga ndi zamathothomathotho.+ 11 Kenako, mngelo wa Mulungu woona anandiitana mʼmalotowo kuti, ‘Yakobo!’ Ine ndinayankha kuti, ‘Ine Ambuye.’
-