Salimo 78:40 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 40 Nthawi zambiri iwo ankamupandukira mʼchipululu,+Ndipo ankamukhumudwitsa mʼchipululumo!+