Numeri 13:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Wa fuko la Efuraimu anali Hoshiya,+ mwana wa Nuni. Numeri 13:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Mayina a amuna amene Mose anawatuma kuti akazonde dzikolo ndi amenewa. Mose anapatsa Hoshiya mwana wa Nuni dzina lakuti Yoswa.*+
16 Mayina a amuna amene Mose anawatuma kuti akazonde dzikolo ndi amenewa. Mose anapatsa Hoshiya mwana wa Nuni dzina lakuti Yoswa.*+