Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 32:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Mukawawonongatu Aiguputo anena kuti, ‘Anali ndi zolinga zoipa powatulutsa mʼdziko lino. Iye amafuna kuti akawaphe kumapiri nʼkuwafafaniza padziko lapansi.’+ Bwezani mkwiyo wanu woyaka motowo, ndipo sinthani maganizo anu ofuna kubweretsera anthu anu tsoka limeneli.

  • Ezekieli 20:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Koma ndinachitapo kanthu chifukwa cha dzina langa kuti lisadetsedwe pamaso pa anthu a mitundu ina kumene ankakhalako.+ Chifukwa ndinachititsa kuti iwo* andidziwe pamaso pa anthu a mitundu inawo pamene ndinawatulutsa* mʼdziko la Iguputo.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena