Deuteronomo 4:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Ndiyeno Yehova anayamba kukulankhulani kuchokera mʼmoto.+ Inu munamva mawu koma simunaone kalikonse.+ Munangomva mawu okha basi.+ Deuteronomo 5:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Yehova analankhula nanu pamasomʼpamaso mʼphiri, kuchokera mʼmoto.+
12 Ndiyeno Yehova anayamba kukulankhulani kuchokera mʼmoto.+ Inu munamva mawu koma simunaone kalikonse.+ Munangomva mawu okha basi.+