Ekisodo 6:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ine ndidzakulowetsani mʼdziko limene ndinalumbira* kuti ndidzalipereka kwa Abulahamu, Isaki ndi Yakobo. Ndidzakupatsani dzikolo kuti likhale lanu.+ Ine ndine Yehova.’”+
8 Ine ndidzakulowetsani mʼdziko limene ndinalumbira* kuti ndidzalipereka kwa Abulahamu, Isaki ndi Yakobo. Ndidzakupatsani dzikolo kuti likhale lanu.+ Ine ndine Yehova.’”+