Numeri 13:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Ndipo iwo anapitiriza kuuza Aisiraeliwo lipoti loipa+ lokhudza dziko limene anakalizondalo kuti: “Dziko limene tinakalizondalo limameza anthu ake, ndipo anthu onse amene tinawaona kumeneko ndi ziphona zamatupi akuluakulu.+
32 Ndipo iwo anapitiriza kuuza Aisiraeliwo lipoti loipa+ lokhudza dziko limene anakalizondalo kuti: “Dziko limene tinakalizondalo limameza anthu ake, ndipo anthu onse amene tinawaona kumeneko ndi ziphona zamatupi akuluakulu.+