Levitiko 24:11, 12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Mnyamatayo anayamba kunyoza* ndi kutukwana dzina la Mulungu.*+ Ndiye anapita naye kwa Mose.+ Dzina la mayi ake linali Selomiti, mwana wa Dibiri wa fuko la Dani. 12 Ndiyeno anamutsekera kudikira kuti Yehova apereke chigamulo pa nkhaniyo.+
11 Mnyamatayo anayamba kunyoza* ndi kutukwana dzina la Mulungu.*+ Ndiye anapita naye kwa Mose.+ Dzina la mayi ake linali Selomiti, mwana wa Dibiri wa fuko la Dani. 12 Ndiyeno anamutsekera kudikira kuti Yehova apereke chigamulo pa nkhaniyo.+