Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 12:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Pomaliza, Samueli anauza Aisiraeli onse kuti: “Ndachita zonse zimene* munandiuza, ndipo ndakusankhirani mfumu yoti izikulamulirani.+

  • 1 Samueli 12:3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 3 Ine ndaima pano. Mupereke umboni pamaso pa Yehova ndi pamaso pa wodzozedwa wake:+ Kodi alipo amene ndinamʼtengera ngʼombe kapena bulu wake?+ Nanga alipo amene ndinamʼchitirapo zachinyengo kapena kumʼpondereza? Kodi ndinalandirapo chiphuphu kwa aliyense kuti ndisachite chilungamo?+ Ngati ndinachitapo zimenezi, ndine wokonzeka kukubwezerani.”+

  • Machitidwe 20:33
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 33 Sindinasirire siliva, golide kapena chovala cha munthu.+

  • 2 Akorinto 7:2
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 2 Titsegulireni mitima yanu.*+ Ifetu sitinalakwire aliyense, sitinaipitse aliyense ndipo sitinadyere aliyense masuku pamutu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2026)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena