Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Numeri 26:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Zitatero, nthaka inangʼambika* nʼkuwameza. Koma Kora anafa pamene moto unapsereza amuna 250.+ Ndipo iwo anakhala chitsanzo chotichenjeza.+

  • Deuteronomo 11:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 kapena zimene anachitira Datani ndi Abiramu, ana a Eliyabu, mwana wa Rubeni, pamene dziko linatsegula pakamwa pake nʼkuwameza pamodzi ndi mabanja awo, matenti awo ndi chamoyo chilichonse chimene anali nacho. Dziko linawameza Aisiraeli onse akuona.+

  • Salimo 106:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Kenako dziko lapansi linatseguka ndipo linameza Datani,

      Nʼkukwirira anthu onse amene anali kumbali ya Abiramu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2026)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena