Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 6:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Mwamuna aliyense mwa ana a Aroni azidya mkatewo.+ Limeneli ndi gawo lawo lochokera pansembe zowotcha pamoto+ zoperekedwa kwa Yehova, mʼmibadwo yanu yonse mpaka kalekale. Chilichonse chimene chingakhudze nsembezi chidzakhala choyera.’”

  • Levitiko 7:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 7 “‘Lamulo la nsembe yakupalamula+ ndi ili: Nsembeyi ndi yopatulika koposa.

  • Levitiko 7:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Mwamuna aliyense yemwe ndi wansembe azidya nyamayo+ ndipo aziidyera mʼmalo oyera. Nsembeyi ndi yopatulika koposa.+

  • Levitiko 14:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Kenako azipha nkhosa yaingʼono yamphongoyo pamalo amene nthawi zonse amapherapo nyama ya nsembe yamachimo ndi nsembe yopsereza,+ pamalo oyera. Azichita zimenezi chifukwa nsembe yakupalamula ndi ya wansembe+ mofanana ndi nsembe yamachimo. Nsembe yakupalamula ndi yopatulika koposa.+

  • Levitiko 21:22
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 22 Iye angathe kudya chakudya cha Mulungu wake kuchokera pa zinthu zopatulika koposa+ ndi pa zinthu zopatulika.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena