Ekisodo 22:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Zimene muzichita ndi mwana woyamba kubadwa wa ngʼombe ndi wa nkhosa yanu ndi izi:+ Azikhala ndi mayi ake masiku 7. Pa tsiku la 8 muzimupereka kwa ine.+ Deuteronomo 15:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Mwana aliyense wamphongo woyamba kubadwa wa ngʼombe kapena wa nkhosa muzimupatula nʼkumupereka kwa Yehova Mulungu wanu.+ Musamagwiritse ntchito iliyonse mwana woyamba kubadwa wa ngʼombe,* kapena kumeta ubweya wa mwana woyamba kubadwa wa nkhosa.
30 Zimene muzichita ndi mwana woyamba kubadwa wa ngʼombe ndi wa nkhosa yanu ndi izi:+ Azikhala ndi mayi ake masiku 7. Pa tsiku la 8 muzimupereka kwa ine.+
19 Mwana aliyense wamphongo woyamba kubadwa wa ngʼombe kapena wa nkhosa muzimupatula nʼkumupereka kwa Yehova Mulungu wanu.+ Musamagwiritse ntchito iliyonse mwana woyamba kubadwa wa ngʼombe,* kapena kumeta ubweya wa mwana woyamba kubadwa wa nkhosa.