Yoswa 13:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Koma fuko la Alevi, Mose sanalipatse cholowa.+ Chifukwa cholowa chawo ndi Yehova Mulungu wa Isiraeli, mogwirizana ndi zimene anawalonjeza.+
33 Koma fuko la Alevi, Mose sanalipatse cholowa.+ Chifukwa cholowa chawo ndi Yehova Mulungu wa Isiraeli, mogwirizana ndi zimene anawalonjeza.+