Levitiko 22:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Uza Aroni ndi ana ake kuti azilemekeza* zinthu zopatulika zimene Aisiraeli abweretsa kwa ine,+ kuti asadetse dzina langa loyera.+ Ine ndine Yehova. Levitiko 22:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Zili choncho kuti ansembe asamadetse zinthu zopatulika za Aisiraeli, zimene amapereka kwa Yehova,+
2 “Uza Aroni ndi ana ake kuti azilemekeza* zinthu zopatulika zimene Aisiraeli abweretsa kwa ine,+ kuti asadetse dzina langa loyera.+ Ine ndine Yehova.
15 Zili choncho kuti ansembe asamadetse zinthu zopatulika za Aisiraeli, zimene amapereka kwa Yehova,+