Ekisodo 17:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Gulu lonse la Aisiraeli linachoka kuchipululu cha Sini.+ Ulendowo anaugawa mʼzigawo, mogwirizana ndi mmene Yehova anawauzira,+ ndipo anamanga msasa ku Refidimu.+ Koma kumeneko kunalibe madzi akumwa.
17 Gulu lonse la Aisiraeli linachoka kuchipululu cha Sini.+ Ulendowo anaugawa mʼzigawo, mogwirizana ndi mmene Yehova anawauzira,+ ndipo anamanga msasa ku Refidimu.+ Koma kumeneko kunalibe madzi akumwa.