Yohane 3:14, 15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mofanana ndi Mose amene anakweza njoka mʼmwamba mʼchipululu,+ Mwana wa munthunso akuyenera kukwezedwa mʼmwamba+ 15 kuti aliyense womukhulupirira akhale ndi moyo wosatha.+
14 Mofanana ndi Mose amene anakweza njoka mʼmwamba mʼchipululu,+ Mwana wa munthunso akuyenera kukwezedwa mʼmwamba+ 15 kuti aliyense womukhulupirira akhale ndi moyo wosatha.+