Yoswa 24:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Kenako Balaki mwana wa Zipori, mfumu ya Mowabu, ananyamuka kukamenyana ndi Aisiraeli. Iye anaitanitsa Balamu, mwana wa Beori kuti akutemberereni.+ Oweruza 11:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 Ndiye iweyo wasiyana pati ndi Balaki+ mwana wa Zipori, mfumu ya Mowabu? Kodi iye anakwanitsa kulimbana ndi Aisiraeli, kapena anayesa nʼkomwe kumenyana nawo?
9 Kenako Balaki mwana wa Zipori, mfumu ya Mowabu, ananyamuka kukamenyana ndi Aisiraeli. Iye anaitanitsa Balamu, mwana wa Beori kuti akutemberereni.+
25 Ndiye iweyo wasiyana pati ndi Balaki+ mwana wa Zipori, mfumu ya Mowabu? Kodi iye anakwanitsa kulimbana ndi Aisiraeli, kapena anayesa nʼkomwe kumenyana nawo?