Ekisodo 6:23 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 23 Aroni anatenga Eliseba, mwana wamkazi wa Aminadabu, mchemwali wake wa Naasoni,+ kukhala mkazi wake. Ndipo Eliseba anamʼberekera Nadabu, Abihu, Eleazara ndi Itamara.+ Ekisodo 38:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Mose analamula kuti awerengere zinthu zonse zimene anagwiritsa ntchito popanga chihema, kapena kuti chihema cha Umboni.+ Alevi ndi amene anachita zimenezi+ motsogoleredwa ndi Itamara+ mwana wa Aroni wansembe. 1 Mbiri 6:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ana a Amuramu+ anali Aroni,+ Mose+ ndi Miriamu.+ Ana a Aroni anali Nadabu, Abihu,+ Eliezara+ ndi Itamara.+
23 Aroni anatenga Eliseba, mwana wamkazi wa Aminadabu, mchemwali wake wa Naasoni,+ kukhala mkazi wake. Ndipo Eliseba anamʼberekera Nadabu, Abihu, Eleazara ndi Itamara.+
21 Mose analamula kuti awerengere zinthu zonse zimene anagwiritsa ntchito popanga chihema, kapena kuti chihema cha Umboni.+ Alevi ndi amene anachita zimenezi+ motsogoleredwa ndi Itamara+ mwana wa Aroni wansembe.
3 Ana a Amuramu+ anali Aroni,+ Mose+ ndi Miriamu.+ Ana a Aroni anali Nadabu, Abihu,+ Eliezara+ ndi Itamara.+