Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 13:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Pofuna kuwatsogolera, Yehova ankayenda patsogolo pawo. Masana ankawatsogolera pogwiritsa ntchito chipilala cha mtambo+ ndipo usiku ankawatsogolera pogwiritsa ntchito chipilala cha moto kuti chiziwaunikira. Choncho ankatha kuyenda masana komanso usiku.+

  • Ekisodo 23:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Ndikukutumizirani mngelo patsogolo panu+ kuti azikutetezani mʼnjira komanso kukakulowetsani mʼdziko limene ndakukonzerani.+

  • Ekisodo 29:45
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 45 Ndidzakhala pakati pa Aisiraeli ndipo ndidzakhala Mulungu wawo.+

  • Yesaya 8:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Konzani pulani, koma idzalephereka.

      Nenani zimene mukufuna, koma sizidzachitika,

      Chifukwa Mulungu ali nafe.*+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena