Numeri 25:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Pinihasi+ mwana wa Eleazara, mdzukulu wa wansembe Aroni, ataona zimenezi nthawi yomweyo ananyamuka pakati pa gululo nʼkutenga mkondo* mʼdzanja lake.
7 Pinihasi+ mwana wa Eleazara, mdzukulu wa wansembe Aroni, ataona zimenezi nthawi yomweyo ananyamuka pakati pa gululo nʼkutenga mkondo* mʼdzanja lake.