Numeri 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Iweyo ndi Aroni muwalembe mʼkaundula mogwirizana ndi magulu awo.* Uwerenge onse kuyambira azaka 20 kupita mʼtsogolo,+ amene ali oyenera kupita kunkhondo mu Isiraeli.
3 Iweyo ndi Aroni muwalembe mʼkaundula mogwirizana ndi magulu awo.* Uwerenge onse kuyambira azaka 20 kupita mʼtsogolo,+ amene ali oyenera kupita kunkhondo mu Isiraeli.